Ezekieli 17:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Unaokedwa mu nthaka yabwino kuli madzi ambiri, kuti uphuke nthambi, nubale zipatso, nukhale mpesa wabwino.

Ezekieli 17

Ezekieli 17:3-15