Ezekieli 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma unatama kukongola kwako, ndi kucita zacigololo potama mbiri yako, ndi kutsanulira zigololo zako pa munthu ali yense wopitapo; unali wace.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:5-17