Ezekieli 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Ambuye Yehova, Kopambana kotani nanga ndikatumizira Yerusalemu maweruzo anga anai owawa, lupanga, njala, zirombo zoipa, ndi mliri, kuudulira anthu ndi nyama?

Ezekieli 14

Ezekieli 14:17-23