Ezekieli 14:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cinkana Nowa, Danieli, ndi Yobu, akadakhala m'mwemo, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, sakadapulumutsa ana amuna kapena akazi; akadapulumutsa moyo wao wokha ndi cilungamo cao.

Ezekieli 14

Ezekieli 14:17-23