Ezekieli 13:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza mwamvetsa cisoni ndi mabodza mtima wa wolungama, amene sindinamvetsa cisoni Ine, ndi kumlimbitsa manja woipa, kuti asabwerere kuleka njira yace yoipa, ndi kusungidwa wamoyo;

Ezekieli 13

Ezekieli 13:19-23