Ezekieli 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zokuta mitu zanu zomwe ndidzazing'amba, ndi kulanditsa anthu anga m'manja mwanu; ndipo sadzakhalanso m'mphamvu mwanu kusakidwa; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 13

Ezekieli 13:20-23