Ezekieli 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace uziti, Atero Yehova Mulungu, Ndidzakumemezani ku mitundu ya anthu, ndi kukusonkhanitsani mucoke m'maiko m'mene munabalalikiramo, ndipo ndidzakuninkhani dziko la Israyeli.

Ezekieli 11

Ezekieli 11:12-19