Ezekieli 11:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace uziti, Atero Yehova Mulungu, Ngakhale ndawacotsa kutali mwa amitundu, ngakhalenso ndawabalalikitsa m'maiko, koma ndidzawakhalira malo opatulika kanthawi ku maiko adafikako.

Ezekieli 11

Ezekieli 11:11-22