Ezara 2:67 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu; aburu zikwi zisanu ndi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.

Ezara 2

Ezara 2:60-70