Ezara 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse akuwazinga analimbitsa manja ao ndi zipangizo za siliva, ndi golidi, ndi cuma, ndi zoweta, ndi zinthu za mtengo wace, pamodzi ndi nsembe zaufulu.

Ezara 1

Ezara 1:4-11