Estere 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nitinso mfumu kwa Estere tsiku laciwirili pa madyerero a vinyo, Pempho lanu nciani, mkazi wamkuru Estere? lidzapatsidwa kwa inu; mufunanji? cidzacitika, kufikira limodzi la magawo awiri a ufumu wanga.

Estere 7

Estere 7:1-9