Eksodo 39:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolidi, naziika pa nsonga ziwiri za capacifuwa, m'mphepete mwace m'katimo, pa mbali ya kuefodi.

Eksodo 39

Eksodo 39:14-24