Eksodo 28:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuyandikire Aroni mbale wako, ndi ana ace amuna pamodzi naye, mwa ana a Israyeli, kuti andicitire Ine nchito ya nsembe, ndiwo Aroni, Nadabu, ndi Abihu, Eleazara ndi ltamara, ana a Aroni.

Eksodo 28

Eksodo 28:1-9