Eksodo 27:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aroni ndi ana ace aikonze m'cihema cokomanako, kunja kwa nsaru yocinga yokhala kumboni, kuyambira madzulo kufikira m'mawa; likhale lemba losatha mwa mibadwo yao, alisunge ana a Israyeli.

Eksodo 27

Eksodo 27:11-21