Eksodo 14:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si awa maowo tinalankhula nanu m'Aigupto ndi kuti, Tliekeni, kuti tigwirire nchito Aaigupto? pakuti kutumikira Aaigupto kutikomera si kufa m'cipululu ai.

Eksodo 14

Eksodo 14:4-14