Eksodo 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa Mose, Kodi mwaticotsera kuti tikafe m'cipululu cifukwa panahbe manda m'Aigupto? Nciani ici mwaticitira kuti mwatiturutsa m'Aigupto?

Eksodo 14

Eksodo 14:3-13