Eksodo 12:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiwo usiku wosungira Yehova ndithu, cifukwa ca kuwaturutsa m'dziko la Aigupto; usiku womwe uno ukhale wosungira Yehova ana onse a Israyeli ku mibadwo yao.

Eksodo 12

Eksodo 12:37-51