Eksodo 12:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunakhala pakutha zaka mazana anai kudza makumi atatu, inde panakhala tsiku lomwelo, makamu onse a Yehova anaturuka m'dziko la Aigupto.

Eksodo 12

Eksodo 12:40-48