Eksodo 12:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaitana Mose ndi Aroni usiku, nati, Ukani, turukani pakati pa anthu anga, inu ndi ana a Israyeli; ndipo mukani katumikireni Yehova, monga mwanena.

Eksodo 12

Eksodo 12:30-40