Eksodo 12:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anauka usiku, iyendi anyamata ace onse, ndi Aaigupto onse; ndipo kunali kulira kwakukulu m'Aigupto; pakuti panalibe nyumba yopanda wakufa m'mwemo.

Eksodo 12

Eksodo 12:27-31