Eksodo 12:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anawerama, nalambira. Ndipo ana a Israyeli anamuka nacita monga Yehova adalamulira Mose ndi Aroni; anacita momwemo.

Eksodo 12

Eksodo 12:27-32