Deuteronomo 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero mudziwe lero lino, kuti Yehova Mulungu wanu ndiye amene aoloka pamaso panu ngati moto wonyeketsa; iye adzawaononga, iye adzawagwetsa pamaso panu; potero mudzawapitikitsa, ndi kuwaononga msanga, monga Yehova analankhula ndi inu.

Deuteronomo 9

Deuteronomo 9:1-7