Deuteronomo 5:16-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Lemekeza atate wako ndi amako, monga Yehova Mulungu wako anakulamulira; kuti masiku ako acuruke, ndi kuti cikukomere, m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.

17. Usaphe.

18. Usacite cigololo.

19. Usabe.

20. Usamnamizire mnzako.

Deuteronomo 5