Deuteronomo 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lemekeza atate wako ndi amako, monga Yehova Mulungu wako anakulamulira; kuti masiku ako acuruke, ndi kuti cikukomere, m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.

Deuteronomo 5

Deuteronomo 5:15-18