Deuteronomo 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzikumbukilakuti unali kapolo m'dziko la Aigupto, ndi kuti Yehova Mulungu wako anakuturutsako ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasuka; cifukwa cace Yehova Mulungu wako anakulamulira kusunga tsiku la Sabata.

Deuteronomo 5

Deuteronomo 5:10-20