Deuteronomo 32:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tapenyani tsopano kuti Ine ndine iye,Ndipo palibe mulungu koma Ine;Ndipha Ine, ndikhalitsanso ndi mayo:Ndikantha, ndicizanso Ine;Ndipo palibe wakulanditsa m'dzanja langa.

Deuteronomo 32

Deuteronomo 32:37-47