Deuteronomo 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Penyani muli mokhalamo mwanu mopatulika, m'mwamba, ndipo dalitseni anthu anu Israyeli, ndi nthaka imene munatipatsa, monga munalumbirira makolo athu, dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.

Deuteronomo 26

Deuteronomo 26:9-19