Deuteronomo 26:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sindinadyako m'cisoni canga, kapena kucotsako podetsedwa, kapena kuperekako kwa akufa; ndamvera mau a Yehova Mulungu wanga; ndacita monga mwa zonse munandilamulira ine.

Deuteronomo 26

Deuteronomo 26:12-19