Deuteronomo 19:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Yehova Mulungu wanu ataononga amitundu, amene Yehova Mulungu wanu akupatsani dziko lao, ndipo mutalilandira lanu lanu, ndi kukhala m'midzi mwao, ndi m'nyumba zao;

Deuteronomo 19

Deuteronomo 19:1-7