Deuteronomo 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mneneri akanena m'dzina la Yehova, koma mau adanenawa sacitika, nisafika, ndiwo mau Yehova sanawanena; mneneriyo ananena modzikuza, musamuopa iye.

Deuteronomo 18

Deuteronomo 18:20-22