Deuteronomo 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muziwaphunzitsa ana anu, ndi kuwalankhula awa pokhala inu pansi m'nyumba mwanu, ndi poyenda inu panjira, ndi pogona inu pansi, ndi pakuuka inu pomwe.

Deuteronomo 11

Deuteronomo 11:11-21