Deuteronomo 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Israyeli, Yehova Mulungu wanu afunanji nanu, koma kuti muziopa Yehova Mulungu wanu, kuyenda m'njira zace zonse, ndi kukonda, ndi kutumikira Yehova Mulungu wanundimtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse,

Deuteronomo 10

Deuteronomo 10:7-15