Deuteronomo 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Uka, tenga ulendo pamaso pa anthu; kuti alowe ndi kulandira dzikoli ndinalumbirira makolo ao kuti ndidzawapatsa.

Deuteronomo 10

Deuteronomo 10:2-13