Danieli 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga mulembedwa m'cilamulo ca Mose coipa ici conse catidzera; koma sitinapepeza Yehova Mulungu wathu, ndi kubwera kuleka mphulupulu zathu, ndi kucita mwanzeru m'coonadi canu.

Danieli 9

Danieli 9:6-23