Danieli 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakwaniritsa mau ace adanenawo, kutitsutsa ife ndi oweruza athu otiweruza, ndi kutitengera coipa cacikuru; pakuti pansi pa thambo lonse sipanacitika monga umo panacitikira Yerusalemu.

Danieli 9

Danieli 9:2-15