Danieli 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mphamvu yace idzakhala yaikuru, koma si mphamvu yace yace ai, nidzaononga modabwiza, nidzakuzika, ndi kucita, ndi kuononga amphamvuwo, ndi anthu opatulikawo.

Danieli 8

Danieli 8:22-25