Danieli 7:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunena za nyanga khumi, m'ufumu uwu adzauka mafumu khumi, ndi pambuyo pao idzauka yina; iyo idzasiyana ndi oyamba aja, nidzacepetsa mafumu atatu.

Danieli 7

Danieli 7:14-28