Danieli 7:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anatero, cirombo cacinai ndico ufumu wacinai pa dziko lapansi, umene udzasiyana nao maufumu onse, nudzalusira dziko lonse lapansi, nudzalipondereza ndi kuliphwanya.

Danieli 7

Danieli 7:17-28