Danieli 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinapenya, ndipo nyanga yomweyi inacita nkhondo ndi opatulikawo, niwalaka, mpaka inadza Nkhalamba ya kale lomwe;

Danieli 7

Danieli 7:11-28