Danieli 7:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi za nyanga khumi zinali pamutu pace, ndi nyanga yina Idaphukayi, imene zidagwa zitatu patsogolo pace; nyangayo idali ndi maso ndi pakamwa pakunena zazikuru, imene maonekedwe ace anaposa zinzace.

Danieli 7

Danieli 7:17-27