Danieli 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka coyamba ca Belisazara mfumu ya ku Babulo Danieli anaona loto, naona masomphenya a m'mtima mwace pakama pace; ndipo analemba lotolo, nalifotokozera, mwacidule.

Danieli 7

Danieli 7:1-7