Danieli 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu wanga watuma mthenga wace, natseka pakamwa pa mikango; ndipo siinandipweteka, cifukwa anandiona wosacimwa pamaso pace, pamaso panunso, mfumu, sindinalakwa.

Danieli 6

Danieli 6:17-24