Danieli 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nebukadinezara anayankha, nati kwa iwo, Kodi mutero dala, Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, kusatumikira milungu yanga, ndi kusalambira fano lagolidi ndinaliimikalo?

Danieli 3

Danieli 3:12-18