Danieli 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Nebukadinezara, mumkwiyo ndi m'ukali wace, anawauza abwere nao Sadrake, Mesake, ndi Abedinego. Ndipo anabwera nao amunawa kwa mfumu.

Danieli 3

Danieli 3:10-22