Danieli 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kuyambira nthawi yoti idzacotsedwa nsembe yacikhalire, nicidzaimika conyansa cakupululutsa, adzakhalanso masiku cikwi cimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.

Danieli 12

Danieli 12:9-12