Danieli 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi milungu yao yomwe, pamodzi ndi akalonga ao, ndi zipangizo zao zofunika za siliva ndi golidi adzazitenga kumka nazo ndende ku Aigupto; ndi zaka zace zidzaposa za mfumu ya kumpoto.

Danieli 11

Danieli 11:1-11