Danieli 11:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma apo pophukira mizu yace adzauka wina m'malo mwace, ndiye adzafika kulimbana nalo khamu la nkhondo, nadzalowa m'linga la mfumu ya kumpoto, nadzacita molimbana nao, nadzawalaka;

Danieli 11

Danieli 11:1-15