Danieli 11:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo aphunzitsi a anthu adzalangiza ambiri, koma adzagwa ndi lupanga, ndi lawi lamoto, ndi undende, ndi kufunkhidwa masiku ambiri.

Danieli 11

Danieli 11:28-36