Danieli 11:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akucitira coipa cipanganoco iye adzawaipsa, ndi kuwasyasyalika; koma anthu akudziwa Mulungu wao adzalimbika mtima, nadzacita mwamphamvu.

Danieli 11

Danieli 11:31-39