Danieli 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mfumu ya kumpoto idzabwera, nidzaimika unyinji wa kuposa oyamba aja; nidzafika pa cimariziro ca nthawi, ca zaka, ndi khamu lalikuru la nkhondo ndi cuma cambiri.

Danieli 11

Danieli 11:11-23